12 months ago
Peer Help.
My girl friend has asked me to choose her or break up.
Nkhani ndiyoti nthawi zonse tikamakuna phone yake amayisiya kwawo samayitenga tsiku ina titakumana pa sewu anabitsa phone anakaniza kuti ndisayione. Takhala tisakuvana pa nkhani ya phone yakeyi kuti amayibisilanji. Dzulo wandiuza kuti ngati ndingakakamile za phone chibwezi chithe. Guyz nditani pamenepa?

lero chaku mawawa ***** i fatsanmw padali pano ndi Aishmw munthu ameneyiyi zikukhala bwanji?
12 months ago
ma banja sakulimba matsiku ano coz most of the people akumalowa m'banja not just bcoz nthawi yawo yakwana yolowa m'banja ayi koma chifukwa cha zilakolako za thupi.ili ndi vuto lalikulu ndithu.Let's think twice before get into marriage.🙏
kodi wachifundo ndani andilipilire ku verified
kodi wachifundo ndani andilipilire ku verified
12 months ago
mwati zikukhala bwanji pa mudzi pano zikundibalalitsa zamasubscribezi tikufunikira maphunziro ndithu😎😎
Sponsored by
Pampanje
11 months ago