Peer Help.
My girl friend has asked me to choose her or break up.
Nkhani ndiyoti nthawi zonse tikamakuna phone yake amayisiya kwawo samayitenga tsiku ina titakumana pa sewu anabitsa phone anakaniza kuti ndisayione. Takhala tisakuvana pa nkhani ya phone yakeyi kuti amayibisilanji. Dzulo wandiuza kuti ngati ndingakakamile za phone chibwezi chithe. Guyz nditani pamenepa?

12 months ago