Logo
Diverson Danger
1 yr. ago
wallet ndawona koma kuti 1pin pachedwatu achina aisha
Diverson Danger
1 yr. ago
Peer Help.
My girl friend has asked me to choose her or break up.
Nkhani ndiyoti nthawi zonse tikamakuna phone yake amayisiya kwawo samayitenga tsiku ina titakumana pa sewu anabitsa phone anakaniza kuti ndisayione. Takhala tisakuvana pa nkhani ya phone yakeyi kuti amayibisilanji. Dzulo wandiuza kuti ngati ndingakakamile za phone chibwezi chithe. Guyz nditani pamenepa?
Diverson Danger
1 yr. ago
FREE MODE Administrator zikut?
Diverson Danger
1 yr. ago
Kodi Free Mode atipeza liti pamudzi pano osaiwala kuno ndikupanjezi
Diverson Danger
1 yr. ago
STOP LIVING FAKE LIFE❗
Diverson Danger
1 yr. ago
lero chaku mawawa ***** i fatsanmw padali pano ndi Aishmw munthu ameneyiyi zikukhala bwanji?
Diverson Danger
1 yr. ago
iwe Aishamw za bho?💗
Diverson Danger
1 yr. ago
ma banja sakulimba matsiku ano coz most of the people akumalowa m'banja not just bcoz nthawi yawo yakwana yolowa m'banja ayi koma chifukwa cha zilakolako za thupi.ili ndi vuto lalikulu ndithu.Let's think twice before get into marriage.🙏

kodi wachifundo ndani andilipilire ku verified
Diverson Danger
1 yr. ago
what makes relationships stay strong? Tatiuzeni Timve Nawo
Diverson Danger
1 yr. ago
NOTHING FOR US WITHOUT US
-follow me-
Diverson Danger
1 yr. ago
mwati zikukhala bwanji pa mudzi pano zikundibalalitsa zamasubscribezi tikufunikira maphunziro ndithu😎😎
Diverson Danger
1 yr. ago
😕😕kodi pano pali madona koma😕
Diverson Danger
1 yr. ago
we are here @mellzkumpanje