8 months ago
When l was a child, l thought like a child. But growing up taught me that not everything we chase has real value. Focus on what truly matters.
Aisha pinned this post
12 months ago
Hello help me πππππππ₯°π₯° follow me please ππππππππππππππ§βπΌπ§βπΌπ§βπΌπ₯°π₯°π
Subscribe to Unlock
For MK100.00 / Monthly
12 months ago
Mwanayu tu si AJuh Koma Zeze. Uyu adali producer mu studio mwa Daredevilz. Ma artist akulu akulu onsewa, Zeze ankawapanga record, GD ******* ixer ma vocals, uku Marcus ma instrumental.
Nkhani ya Zeze ukayimva, ngati sewero la tikufelanji
Nkhani ya Zeze ukayimva, ngati sewero la tikufelanji
12 months ago
Kulowa Mkati Sikudali Kophweka. Welcome to Maula Prison Movie yatsala pangβono kuonetsedwa πΏ
[ π· Amuna Achisale ali mkati ]
[ π· Amuna Achisale ali mkati ]
12 months ago
12 months ago
Aka nkoyamba AJuh kufika 100K views in 1 Day. Congratulations mwana iwe AJuh guffi π
Ili pa repeat https://youtu.be/oi2EPa_E2...
Ili pa repeat https://youtu.be/oi2EPa_E2...
12 months ago
Movie yatha ndipo anthu ayamika kuti ntchito yagwilidwa. Mawa ku Mount Soche ndipo Sunday ku Mzuzu πππ Ena idzatipeza pa yuchubu
12 months ago
Phalombe Sweetness yafika pa Theba πΏπ¦
Atsikana omwe abhebhesa ntchito zaku bedi mma banja 'Tomaida and Marcelline' akuziwisa aMalawi kujoni kuti pakadali pano ali ku Capetown ndipo sunday apezekela ku Jo'burg. Kwa amene afuna kulumikizana nawo ******* kuwayimbila pa +27754842655
Atsikana omwe abhebhesa ntchito zaku bedi mma banja 'Tomaida and Marcelline' akuziwisa aMalawi kujoni kuti pakadali pano ali ku Capetown ndipo sunday apezekela ku Jo'burg. Kwa amene afuna kulumikizana nawo ******* kuwayimbila pa +27754842655
12 months ago
Unconsciously, another week has come to an end. Today, I read a very interesting book called "The Simple Path to Wealth". My favorite sentence in the book is: If you just do nothing, since even if someone wants to help you, they can't help you, then you will never find the way to success and live an ordinary and poor life. As Warren Buffett said: "If you don't find a way to make money while you sleep, you will work until you die." It sounds cold, but it does remind us that while working hard, we must also think about the longer-term future. this weekend is both relaxing and fulfilling. Good morning everyone.#pampanje #boswell24e #onlinework24e #b24Γ¨
Subscribe to Unlock
For MK100.00 / Monthly
12 months ago
Nde posachedwapa muona asing'anga ayambapo pa platform ino amvekere
Ine ndine doctor chakutichakuti
Eiish atikwanat
#DionMultimedia
@mellzkumpanje
Ine ndine doctor chakutichakuti
Eiish atikwanat
#DionMultimedia
@mellzkumpanje
Subscribe to Unlock
For MK50.00 / Monthly