Logo
Mikozi
1 yr. ago
GOODMORNING ☀️
Mikozi
1 yr. ago
Usiku watha ku Mzimba show ya Gwamba supported by Emmie Deebo and Lady Aika sim’mene kunaliri
Mikozi
1 yr. ago
Sunday Morning Verse [ Yesaya 4:1 ]

Tsiku limenelo akazi asanu ndi awiri adzagwira mwamuna mmodzi,
nʼkunena kuti, “Ife tizidya chakudya chathuchathu,
ndi kuvala zovala zathu;
inu mungotilola kuti tidziyitanidwa ndi dzina lanu.
Tichotseni manyazi aumbeta!”

GOODMORNING ☀️
Mikozi
1 yr. ago
Kulowa Mkati Sikudali Kophweka. Welcome to Maula Prison Movie yatsala pang’ono kuonetsedwa 🍿

[ 📷 Amuna Achisale ali mkati ]
Mikozi
1 yr. ago
Zakwiyitsa anthu :- President Donald Trump posted an AI-generated image of himself as the Pope
Mikozi
1 yr. ago
NO TIME FI WASTE-: Newly signed artist under porch time records, Oana will drop her first song under the label this Monday.
Mikozi
1 yr. ago
Onesimus One Man Concert Official Set List is Out 🎙️

Usiku uno ku Capetown, African ******* er akaswa nyimbo 20 izi Nonstop
Mikozi
1 yr. ago
Team ya Welcome to Maula Prison tsopano ili mu Blantyre ndipo usiku uno ntchito ilipo ku Mount Soche 🎥
Mikozi
1 yr. ago
Happy 25th Anniversary to Pastor Steven and Pastor Zipporah ( Founders of Zipporah International Foundation ).

Dzaka 25 ali limodzi. Chinsinsi chawo chili pati ?

25th Silver Jubilee Anniversary
Mikozi
1 yr. ago
Nachimalaya Namadingo, Temwa, Beejay & Ace ****** y, Joe Ikon, Crispy Mw, SlyC , and Sean Morgan are ready and set to perform at the MO626 intercollege show happening at Luanar ( Bunda Campus ) tonight !
Mikozi
1 yr. ago
“ Amene munapita ku Premiere sikuti muyambe kutifokozela m’mene zinalili. Mukambilane konko ndipo mutisiye apa YouTube Nafe tidzakambilana “ - Anthu M'ma Group 🍿
Mikozi
1 yr. ago
Mwanayu tu si AJuh Koma Zeze. Uyu adali producer mu studio mwa Daredevilz. Ma artist akulu akulu onsewa, Zeze ankawapanga record, GD ******* ixer ma vocals, uku Marcus ma instrumental.

Nkhani ya Zeze ukayimva, ngati sewero la tikufelanji
Mikozi
1 yr. ago
Happy Sabbath 🙏
GOODMORNING ☀️
Mikozi
1 yr. ago
Gululu ndi Phwedo

[ 📸 Amuna Achisale pa Makina ]
Mikozi
1 yr. ago
Movie yatha ndipo anthu ayamika kuti ntchito yagwilidwa. Mawa ku Mount Soche ndipo Sunday ku Mzuzu 👏👏👏 Ena idzatipeza pa yuchubu
Mikozi
1 yr. ago
Aka nkoyamba AJuh kufika 100K views in 1 Day. Congratulations mwana iwe AJuh guffi 👏

Ili pa repeat https://youtu.be/oi2EPa_E2...
Mikozi
1 yr. ago
Phalombe Sweetness yafika pa Theba 🇿🇦

Atsikana omwe abhebhesa ntchito zaku bedi mma banja 'Tomaida and Marcelline' akuziwisa aMalawi kujoni kuti pakadali pano ali ku Capetown ndipo sunday apezekela ku Jo'burg. Kwa amene afuna kulumikizana nawo ******* kuwayimbila pa +27754842655
Mikozi
1 yr. ago
Zikuoneka kuti Azibambo ena aduka ndikutsekedwa kwa page ya madam Triephonia Mpinganjira
Mikozi
1 yr. ago
‘HOW TO MAKE MONEY GROW ON TREES’ 📕

👆🏽 ili ndi Buku latsopano limene walemba Tendai Shaba ndipo latuluka

Pofokotokoza za zimene zili mu buku li, iye adalankhula mchizungu nati “ We’re still behind on educating our hardworking Malawians about financial literacy and personal finance. This book is all about how we can grow the little we make “ - Watero International Author, Tendai

Buku lo likupezeka apa https://shorturl.at/WJofC
Mikozi
1 yr. ago
Mpakana waika tattoo ya map Malawi. teddy
Mikozi
1 yr. ago
AMatumbi afika ku BICC

[ 📸 Amuna Achisale pa mtchini ]
Mikozi
1 yr. ago
Kulowa Mkati Sikudali Kophweka. Welcome to Maula Prison Movie yatsala pang’ono kuonetsedwa 🍿

[ 📷 Amuna Achisale ali mkati ]
Mikozi
1 yr. ago
“ The people I call my parents today aren’t my biological parents. They adopted me and have raised me for over 20 years. They are the Mundias and I am Mulenga “ - Zambian superstar, Yo Maps reveals

Yo Maps says he never saw his biological Dad who died while he was still a baby. His mother later died while he was very young. That’s when he was adopted by the Mundias.

Akati Mwana wa Mzako ndi Wako emwe. Lero makolo awa waamangila ma mansion

Warning: PHP Request Shutdown: Write failed: Disk quota exceeded (122) in Unknown on line 0

Warning: PHP Request Shutdown: Failed to write session data (files). Please verify that the current setting of session.save_path is correct (/opt/alt/php84/var/lib/php/session) in Unknown on line 0