Nthawi imene Grace China amamwalira iweyo nkuti uli moyo bwanji Sunaulure nthawi imeneyo chifkwa unali mgulu LA Bushiri?
Anthu ngt inuyo ndiamene mukumafna kumationa kupusa aMalawi mmadikila muyambane kotamba kwanuko mukatero muzibwela pano fwe fwe fwe, Mukuganiza kt Azbale ake a Grace akamamva zopusa zanuzo azmva bwanji?
Lero nonsenu mupezeke ku Live Zaka TV Channel tikufunseni mafunso nonsenu Prophet Shepherd Bushiri, Miracle Chinga naweso usalephere kt tidziwe mmene imfa ya Mai ako inayendela
Pamene patsalire bweyapo ifeyo tiponya khala LA moto anthu azmvera fungo
By Zaka

Subscribe to Unlock
For MK50.00 / Monthly
8 days ago