Logo
DSeven Smith
KODI MUKUDZIWA INU?

Nkhuku yakuda ya ku Indonesia ndi yodabwitsa kwambiri, yamtengo wapatali komanso yosowa kwambiri padziko lonse lapansi, imatchedwa "Nkhuku ya Lamborghini", ndipo ndiya breed ya Ayam Cemani.

Mtengo wa mazira ake ukhoza kufika ma dollar 16 pamene nkhuku yayikulu imatha kugulidwa ma dollar 9, 000 'ndipo ndi zokoma kwambiri'".

Chilichonse cha nkhukuyi ndi chakuda, nthenga, milomo, lilime, misomali, ngakhale nyama, mazira ndi mafupa ake. Ponena za magazi ake, ndi ofiira kwambiri, omwe amakhala akuda.

Pangani follow DSeven Smith kuti zina zisakuphonyeni
Subscribe to Unlock

For MK500.00 / Monthly

1 yr. ago

No replys yet!

It seems that this publication does not yet have any comments. In order to respond to this publication from DSeven Smith, click on at the bottom under it


Warning: PHP Request Shutdown: Write failed: Disk quota exceeded (122) in Unknown on line 0

Warning: PHP Request Shutdown: Failed to write session data (files). Please verify that the current setting of session.save_path is correct (/opt/alt/php84/var/lib/php/session) in Unknown on line 0